Marko 14:65 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ena mayamba kumthira malobvu Iye, adi kuphimba nkhope yace, ndi cumbwanyula, ndi kunena naye, Lota; ndipo anyamatawo ananpanda Iye kofu.

Marko 14

Marko 14:58-69