Marko 14:61 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma anakhala cete, osayankhakanthu. Mkulu wa ansembe anamfunsanso, nanena naye, Kodi Iwe ndiwe Kristu, Mwana wace wa Wolemekezeka?

Marko 14

Marko 14:60-69