Marko 14:47 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mmodzi wina wa iwo akuimirirapo, anasolola lupanga lace, nakantha kapolo wace wa mkulu wa ansembe, namdula khutu lace.

Marko 14

Marko 14:42-48