Marko 14:41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anadza kacitatu, nanena nao, Gonani tsopano, nimupumule; cakwanira; yafika nthawi; onani Mwana wa munthu aperekedwa m'manja a anthu ocimwa.

Marko 14

Marko 14:33-51