Marko 14:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Mwana wa munthu amukadi, monga kwalembedwa za Iye; koma tsoka munthuyo amene apereka Mwana wa munthu! Kukadakhala bwino kwa munthu ameneyo ngati sakadabadwa iye.

Marko 14

Marko 14:11-28