Marko 13:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Monga ngati munthu wa paulendo, adacoka kunyumba kwace, nawapatsa akapolo ace ulamuliro, kwa munthu ali yense nchito yace, nalamulira wapakhomo adikire.

Marko 13

Marko 13:27-37