Marko 12:43 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaitana ophunzira ace, nati kwa iwo, Ndithu ndinena ndi inu, Mkazi wamasiye amene waumphawi anaponya zambiri koposa onse akuponya mosungiramo:

Marko 12

Marko 12:41-44