Marko 12:41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Iye anakhala pansi pandunji pa mosungiramo zopereka, napenya kuti khamu la anthu alikuponya ndalama mosungiramo; ndipo eni cuma ambiri anaponyamo zambiri.

Marko 12

Marko 12:40-44