Marko 10:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ophunzirawo anazizwa ndithu ndi mau ace. Koma Yesu anayankhanso nanena nao, Ananu, nkobvuta ndithu kwa iwo akutama cuma kulowa mu Ufumu wa Mulungu!

Marko 10

Marko 10:20-31