Maliro 4:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ophedwa ndi lupanga amva bwino kupambana ophedwa ndi njala;Pakuti amenewa angokwalika napyozedwa, posowa zipatso za m'munda.

Maliro 4

Maliro 4:2-17