Maliro 4:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Angakhale ankhandwe amapatsa bere, nayamwitsa ana ao;Koma mwana wamkazi wa anthu amtundu wanga wasanduka wankhanza, ngati nthiwatiwa za m'cipululu.

Maliro 4

Maliro 4:1-4