Maliro 4:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wodzozedwa wa Yehova, ndiye mpweya wa m'mphuno mwathu, anagwidwa m'maenje ao; Amene tinanena kuti, Tidzakhala m'mthunzi mwace pakati pa amitundu,

Maliro 4

Maliro 4:12-22