Maliro 1:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa ca zimenezi ndilira; diso langa, diso langatu likudza madzi:Pakuti wonditonthoza, wotsitsimutsa moyo wanga, anditarikira;Ana anga asungulumwa, pakuti adaniwo apambana.

Maliro 1

Maliro 1:12-17