Macitidwe 9:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo onse amene anamva anadabwa, nanena, Suyu iye amene anaononga m'Yerusalemu onse akuitana pa dzina ili? Ndipo wadza kuno kudzatero, kuti amuke nao omangidwa kwa ansembe akuru.

Macitidwe 9

Macitidwe 9:11-29