Macitidwe 8:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma panali munthu dzina lace Simoni amene adacita matsenga m'mudzimo kale, nadabwitsa anthu a Samariya, ndi kunena kuti iye yekha ndiye munthu wamkuru;

Macitidwe 8

Macitidwe 8:2-19