Macitidwe 8:3-5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. Ndipo Saulo anapasula Mpingo, nalowa m'nyumba m'nyumba, nakokamo amuna ndi akazi, nawaika m'ndende.

4. Pamenepo ndipo iwo akubalalitsidwa anapitapita nalalikira mauwo.

5. Ndipo Filipo anatsikira ku mudzi wa ku Samarlya, nawalalikira iwo Kristu.

Macitidwe 8