Macitidwe 8:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Simoni mwini wace anakhulupiranso: ndipo m'mene anabatizidwa, anakhalira ndi Filipo; ndipo pakuona zizindikilo ndi mphamvu zazikuru zirikucitika, anadabwa.

Macitidwe 8

Macitidwe 8:11-16