Macitidwe 7:59-60 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

59. Ndipo anamponya miyala Stefano, alikuitana Ambuye, ndi kunena, 29 Ambuye Yesu, landirani mzimu wanga.

60. Ndipo m'mene anagwada pansi, anapfuula ndi mau akuru, 30 Ambuye, musawaikire iwo cimo ili. Ndipo m'mene adanena ici, anagona tulo.

Macitidwe 7