Macitidwe 7:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo anawanyamula kupita nao ku Sukemu, nawaika m'manda amene Abrahamu adagula ndi mtengo wace wa ndalama kwa ana a Emori m'Sukemu.

Macitidwe 7

Macitidwe 7:14-23