Macitidwe 6:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mau a Mulungu anakula; ndipo ciwerengero ca akuphunzira cidacurukatu ku Yerusalemu; ndipo khamu lalikuru la ansembe linamvera cikhulupiriroco.

Macitidwe 6

Macitidwe 6:1-14