Macitidwe 5:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Petro anati kwa iye, Munapangana pamodzi bwanji kuyesa Mzimu wa Ambuye? Taona, mapazi ao a iwo amene anaika mwamuna wako ali pakhomo, ndipo adzakunyamula kuturuka nawe.

Macitidwe 5

Macitidwe 5:8-12