Macitidwe 5:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti asanafike masiku ana anauka Teuda, nanena kuti ali kanthu iye mwini; amene anthu anaphatikana naye, ciwerengero cao ngati mazana anai; ndiye anaphedwa; ndi onse amene anamvera iye anamwazika, napita pacabe.

Macitidwe 5

Macitidwe 5:26-39