Macitidwe 5:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nanena, Tidakulamulirani cilamulire, musaphunzitsa kuchula dzina ili; ndipo taonani, mwadzaza Yerusalemu ndi ciphunzitso canu, ndipo mufuna kutidzetsera ife mwazi wa munthu uja.

Macitidwe 5

Macitidwe 5:26-34