Macitidwe 5:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo atamva ici, analowa m'Kacisi mbanda kuca, naphunzitsa. Koma anadza mkulu wa ansembe ndi iwo amene analinaye, nasonkhanitsa a bwalo la akuru, ndi akulu onse a ana a Israyeli, natuma kundende atengedwe ajawo.

Macitidwe 5

Macitidwe 5:20-27