Macitidwe 5:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Komanso unasonkhana pamodzi unyinji wa anthu ocokera ku midzi yozungulira Yerusalemu, alikutenga odwala, ndi obvutika ndi mizimu yonyansa; ndipo anaciritsidwa onsewa.

Macitidwe 5

Macitidwe 5:10-22