Macitidwe 4:36-37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

36. Ndipo Yosefe, wochedwa ndi atumwi Bamaba (ndilo losandulika mwana wa cisangalalo), Mlevi, pfuko lace la ku Kupro,

37. pokhala nao munda, anaugulitsa, nabwera nazo ndalama zace, 3 naziika pa mapazi a atumwi.

Macitidwe 4