Macitidwe 4:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma pakuona kulimbika mtima kwa Petro ndi Yohane, ndipo pozindikira kuti ndiwo anthu osaphunzira ndi opulukira, anazizwa ndipo anawazindikira, kuti adakhala pamodzi ndi Yesu.

Macitidwe 4

Macitidwe 4:4-20