Macitidwe 4:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Koma m'mene analikulankhula ndi anthu, ansembe ndi mdindo wa kuKacisi ndi Asaduki anadzako,

2. obvutika mtima cifukwa anaphunzitsa anthuwo, nalalikira mwa Yesu kuuka kwa akufa.

Macitidwe 4