Macitidwe 3:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Inu ndinu ana a aneneri, ndi a panganolo Mulungu anapangana ndi makolo anu ndi kunena kwa Abrahamu, Ndipo mu mbeu yako mafuko onse a dziko adzadalitsidwa.

Macitidwe 3

Macitidwe 3:15-26