Macitidwe 28:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunatero kuti atate wace wa Popliyo anagona wodwala nthenda ya malungo ndi kamwazi. Kwa iyeyu Paulo analowa, napemphera, naika manja pa iye, namciritsa.

Macitidwe 28

Macitidwe 28:4-10