Macitidwe 28:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo titapulumuka, pamenepo tinadziwa kuti cisumbuco cinachedwa Melita.

2. Ndipo akunja anaticitira zokoma zosacitika pena ponsepo; pakuti anasonkha moto, natilandira ife tonse, cifukwa ca mvula inalinkugwa, ndi cifukwa ca cisanu.

Macitidwe 28