Macitidwe 27:41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma pofika pamalo pokomana mafunde awiri, anatsamitsapo ngalawa; ndipo kulikuru kunatsama, ndi kukhala kosasunthika, koma kumakaliro kunasweka ndi mphamvu ya mafunde.

Macitidwe 27

Macitidwe 27:34-44