Macitidwe 27:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo popeza kulinkuca, Paulo anawacenjeza onse adye kanthu, nati, Lero ndilo tsiku lakhumi ndi cinai limene munalindira, ndi kusala cakudya, osalawa kanthu.

Macitidwe 27

Macitidwe 27:29-42