Macitidwe 27:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace, limbikani mtima, amuna inu; pakuti ndikhulupirira Mulungu, kuti kudzatero monga momwe ananena ndi ine.

Macitidwe 27

Macitidwe 27:22-28