Macitidwe 26:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Paulo anati, Mwenzi atalola Mulungu, kuti ndi kukopa pang'ono, kapena ndi kukopa kwambiri, si inu nokha, komatunso onse akundimva ine lero, akadakhala otero onga ndiri ine, osanena nsinga izi.

Macitidwe 26

Macitidwe 26:25-32