Macitidwe 26:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo pothandizidwa ndi Mulungu, ndiimirira kufikira lero lino, ndi kuwacitira umboni ang'ono ndi akuru, posanena kanthu kena koma zimene aneneri ndi Mose ananenazidzafika;

Macitidwe 26

Macitidwe 26:15-26