Macitidwe 26:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Komatu uka, imirira pa mapazi ako; pakuti cifukwa ca ici ndinaonekera kwa iwe, kukuika iwe ukhale mtumiki ndi mboni ya izi wandionamo Ine, ndiponso ya izi ndidzakuonekeramo we;

Macitidwe 26

Macitidwe 26:10-18