Macitidwe 26:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene tidagwa pansi tonse, ndinamva mau akunena kwa ine m'cinenedwe ca Cihebri, Saulo, Saulo, undilondalonderanji Ine? nkukubvuta kutsalima pacothwikira.

Macitidwe 26

Macitidwe 26:8-22