Macitidwe 25:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace, ati, iwo amene akhoza mwa inu amuke nane potsikirako, ndipo ngati kuli kanthu kosayenera mwa munthuyo amnenere iye.

Macitidwe 25

Macitidwe 25:3-8