Macitidwe 25:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Potero, pamene adasonkhana pano, sindinacedwa, koma m'mawa mwace ndinakhala pa mpando waciweruziro, ndipo ndinalamulira adze naye munthuyo.

Macitidwe 25

Macitidwe 25:10-25