Macitidwe 24:26-27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

26. Anayembekezanso kuti Paulo adzampatsa ndalama; cifukwa cacenso anamuitana iye kawiri kawiri, nakamba naye.

27. Koma zitapita zaka ziwiri Porkiyo Festo analowa m'malo a Felike; ndipo Felike pofuna kukonda Ayuda anamsiya Paulo m'nsinga.

Macitidwe 24