Macitidwe 24:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ici ndibvomera kwa inu, kuti monga mwa Njira yonenedwa mpatuko, momwemo nditumikira Mulungu wa makolo athu, ndi kukhulupira zonse ziri monga mwa cilamulo, ndi zolembedwa mwa aneneri;

Macitidwe 24

Macitidwe 24:5-24