Macitidwe 22:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinayankha, Ndinu yani Mbuye? Ndipo anati kwa Ine, Ndine Yesu wa ku Nazarete, amene umlondalonda.

Macitidwe 22

Macitidwe 22:1-9