Macitidwe 22:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma m'mawa mwace pofuna kuzindikira cifukwa cace ceni ceni cakuti anamnenera Ayuda, anammasula iye, nalamulira asonkhane ansembe akulu, ndi bwalo lonse la akulu, ndipo anatsika naye Paulo, namuika pamaso pao.

Macitidwe 22

Macitidwe 22:28-30