Macitidwe 22:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo pamene anakhetsa mwazi wa Stefano mboni yanu, ine ndemwe ndinalikuimirirako, ndi kubvomerezana nao, ndi kusunga Zoobvala za iwo amene anamupha iye.

Macitidwe 22

Macitidwe 22:18-26