Macitidwe 21:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mawa mwace tinacoka, ntinafika ku Kaisareya, ndipo m'mene tinalowa m'nyumba ya Filipo mlaliki, mmodzi wa asanu ndi awiri aja, tinakhala naye.

Macitidwe 21

Macitidwe 21:5-15