Macitidwe 21:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene anazimva, analemekeza Mulungu; nati kwa iye, Uona, mbale, kuti ambirimbiri mwa Ayuda akhulupira; ndipo ali naco cangu onsewa, ca pa cilamulo;

Macitidwe 21

Macitidwe 21:13-28