Macitidwe 21:14-16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

14. Ndipo pokana iye kukopeka, tinaleka, ndi kuti, Kufuna kwa Ambuye kucitidwe.

15. Ndipo atapita masiku awa tinakonza akatundu athu, ntikwera ku Yerusalemu.

16. Ndipo anamuka nafenso ena a ophunzira a ku Kaisareya, natenganso wina Mnaso wa ku Kupro, wophunzira wakale, amene adzaticereza.

Macitidwe 21