Macitidwe 21:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Paulo anayankha, Mucitanji, polira ndi kundiswera mtima? pakuti ndakonzeka Ine si kumangidwa kokha, komatunso kufera ku Yerusalemu cifukwa ca dzina la Ambuye Yesu.

Macitidwe 21

Macitidwe 21:5-17