Macitidwe 20:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano ndikuikizani kwa Mulungu, ndi kwa mau a cisomo cace, cimene ciri ndi mphamvu yakumangirira ndi kupatsa inu colowa mwa onse oyeretsedwa.

Macitidwe 20

Macitidwe 20:31-38